Masalimo 72:7 - Buku Lopatulika7 Masiku ake wolungama adzakhazikika; ndi mtendere wochuluka, kufikira sipadzakhala mwezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Masiku ake wolungama adzakhazikika; ndi mtendere wochuluka, kufikira sipadzakhala mwezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pa masiku ake chilungamo chidzakula, mtendere udzachuluka, mpaka mwezi utaleka kuŵala! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mʼmasiku a munthu wolungama adzakhazikika; chuma chidzachuluka mpaka mwezi utaleka kuwala. Onani mutuwo |