Masalimo 72:4 - Buku Lopatulika4 Adzaweruza ozunzika a mwa anthu, adzapulumutsa ana aumphawi, nadzaphwanya wosautsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Adzaweruza ozunzika a mwa anthu, adzapulumutsa ana aumphawi, nadzaphwanya wosautsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mfumu idzateteza anthu osauka, idzapulumutsa anthu osoŵa, koma idzaononga anthu ozunza anzao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iye adzateteza ozunzika pakati pa anthu ndi kupulumutsa ana a anthu osowa; adzaphwanya ozunza anzawo. Onani mutuwo |