Masalimo 72:3 - Buku Lopatulika3 Mapiri adzatengera anthu mtendere, timapiri tomwe, m'chilungamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mapiri adzatengera anthu mtendere, timapiri tomwe, m'chilungamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mapiri adzabweretsa madalitso kwa anthu, magomo adzadzetsa mphotho ya chilungamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mapiri adzabweretsa chuma kwa anthu anu, timapiri tidzabweretsa zipatso zachilungamo. Onani mutuwo |