Masalimo 72:2 - Buku Lopatulika2 Potero adzanenera anthu anu mlandu ndi m'chilungamo, ndi ozunzika anu ndi m'chiweruzo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Potero adzanenera anthu anu mlandu ndi m'chilungamo, ndi ozunzika anu ndi m'chiweruzo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Motero mfumuyo idzaweruza anthu anu molungama ndiponso anthu anu osauka mosakondera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye adzaweruza anthu anu mwachilungamo, anthu anu ozunzika mosakondera. Onani mutuwo |