Masalimo 72:1 - Buku Lopatulika1 Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu, ndi mwana wa mfumu chilungamo chanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu, ndi mwana wa mfumu chilungamo chanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu, patsaniko mfumu nzeru zoweruzira, patsaniko mwana wa mfumu mtima wokonda chilungamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patsani mwana wa mfumu nzeru zanu zoweruzira mwa chilungamo, Inu Mulungu mupatseni mwana wa mfumu chilungamo chanu. Onani mutuwo |