Masalimo 71:24 - Buku Lopatulika24 Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsiku lonse ndidzasimba za kulungama kwanu, pakuti amene ankafuna kundichita choipa, aŵachititsa manyazi ndipo aŵanyazitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Lilime langa lidzafotokoza za ntchito zanu zachilungamo tsiku lonse, pakuti iwo amene amafuna kundipweteka achititsidwa manyazi ndi kusokonezedwa. Onani mutuwo |