Masalimo 72:13 - Buku Lopatulika13 Adzachitira nsoni wosauka ndi waumphawi, nadzapulumutsa moyo wa aumphawi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Adzachitira nsoni wosauka ndi waumphawi, nadzapulumutsa moyo wa aumphawi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Idzamvera chisoni anthu ofooka ndi osoŵa, ndipo idzapulumutsa moyo wa anthu aumphaŵi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye adzachitira chifundo anthu ofowoka ndi anthu osowa ndi kupulumutsa osowa ku imfa. Onani mutuwo |