Masalimo 67:1 - Buku Lopatulika1 Atichitire chifundo Mulungu, ndi kutidalitsa, atiwalitsire nkhope yake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Atichitire chifundo Mulungu, ndi kutidalitsa, atiwalitsire nkhope yake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu mutikomere mtima ndi kutidalitsa, mutiwunikire ndi chikondi chanu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova atikomere mtima ndi kutidalitsa, achititse kuti nkhope yake itiwalire. Onani mutuwo |