Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 66:20 - Buku Lopatulika

20 Wolemekezeka Mulungu, amene sanandipatutsire ine pemphero langa, kapena chifundo chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Wolemekezeka Mulungu, amene sanandipatutsire ine pemphero langa, kapena chifundo chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Mulungu atamandike chifukwa sadakane pemphero langa, sadachotse chikondi chake chosasinthika kwa Ine.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Matamando akhale kwa Mulungu amene sanakane pemphero langa kapena kuletsa chikondi chake pa ine!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 66:20
6 Mawu Ofanana  

Pakuti sanapeputse ndipo sananyansidwe ndi zunzo la wozunzika; ndipo sanambisire nkhope yake; koma pomfuulira Iye, anamva.


Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundichotsa pamaso panu. Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinafuulira kwa Inu.


Musanditaye kundichotsa pamaso panu; musandichotsere Mzimu wanu Woyera.


Inu Mulungu, ndinu woopsa m'malo oyera anu; Mulungu wa Israele ndiye amene apatsa anthu ake mphamvu ndi chilimbiko. Alemekezeke Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa