Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 66:19 - Buku Lopatulika

19 Koma Mulungu anamvadi; anamvera mau a pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Koma Mulungu anamvadi; anamvera mau a pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Koma zoonadi, Mulungu wandimvera, wasamala mau a pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 koma ndithu Mulungu wamvetsera ndipo watchera khutu ku mawu a kupempha kwanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 66:19
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova anati kwa iye, Ndamva pemphero lako ndi pembedzero lako wandipembedza nalo; ndapatula nyumba imene waimangayi kuikamo dzina langa nthawi zosatha, ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala kumeneko masiku onse.


Munthu uyu wozunzika anafuula, ndipo Yehova anamumva, nampulumutsa m'masautso ake onse.


Wamva Yehova kupemba kwanga; Yehova adzalandira pemphero langa.


Ameneyo, m'masiku a thupi lake anapereka mapemphero ndi mapembedzero pamodzi ndi kulira kwakukulu ndi misozi kwa Iye amene anakhoza kumpulumutsa Iye muimfa, ndipo anamveka popeza anaopa Mulungu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa