Masalimo 66:18 - Buku Lopatulika18 Ndikadasekera zopanda pake m'mtima mwanga, Ambuye sakadamvera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndikadasekera zopanda pake m'mtima mwanga, Ambuye sakadamvera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndikadazindikira choipa chilichonse mumtima mwanga ndi kuchibisa, Ambuye sakadandimvera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndikanasekerera tchimo mu mtima mwanga Ambuye sakanamvera; Onani mutuwo |