Masalimo 66:17 - Buku Lopatulika17 Ndinamfuulira Iye pakamwa panga, ndipo ndinamkuza ndi lilime langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndinamfuulira Iye pakamwa panga, ndipo ndinamkuza ndi lilime langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Ndidafuula kwa Iye, ndipo ndidamtamanda ndi pakamwa panga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndinafuwula kwa Iye ndi pakamwa panga, matamando ake anali pa lilime panga. Onani mutuwo |