Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 66:16 - Buku Lopatulika

16 Idzani, imvani, inu nonse akuopa Mulungu, ndipo ndidzafotokozera zonse anazichitira moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Idzani, imvani, inu nonse akuopa Mulungu, ndipo ndidzafotokozera zonse anazichitira moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Bwerani mudzamve, inu nonse amene opembedza Mulungu, ndidzakusimbireni zimene Iye wandichitira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Bwerani ndipo mudzamve inu nonse amene mumaopa Mulungu. Ndidzakuwuzani zimene Iyeyo wandichitira.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 66:16
14 Mawu Ofanana  

Idzani ananu ndimvereni ine, ndidzakulangizani zakumuopa Yehova.


Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera.


Idzani, muone ntchito za Mulungu; zochitira Iye ana a anthu nzoopsa.


Pakamwa panga padzafotokozera chilungamo chanu, ndi chipulumutso chanu tsiku lonse; pakuti sindidziwa mawerengedwe ake.


Poteronso pokalamba ine ndi kukhala nazo imvi musandisiye, Mulungu; kufikira nditalalikira mbadwo uwu za dzanja lanu, mphamvu yanu kwa onse akudza m'mbuyo.


Inu, amene munationetsa nsautso zambiri ndi zoipa, mudzatipatsanso moyo, ndi kutitenganso munsi mwa dziko.


Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma.


Yehova watulutsa chilungamo chathu; tiyeni tilalikire mu Ziyoni ntchito ya Yehova Mulungu wathu.


Pamenepo iwo akuopa Yehova analankhulana wina ndi mnzake; ndipo Yehova anawatchera khutu namva, ndi buku la chikumbutso linalembedwa pamaso pake, la kwa iwo akuopa Yehova, nakumbukira dzina lake.


chimene tidachiona, ndipo tidachimva, tikulalikirani inunso, kuti inunso mukayanjane pamodzi ndi ife; ndipo chiyanjano chathu chilinso ndi Atate, ndipo ndi Mwana wake Yesu Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa