Masalimo 65:2 - Buku Lopatulika2 Wakumva pemphero Inu, zamoyo zonse zidzadza kwa Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Wakumva pemphero Inu, zamoyo zonse zidzadza kwa Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Inu amene mumamvera pemphero, anthu onse adzabwera kwa Inu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Inu amene mumamva pemphero, kwa inu anthu onse adzafika. Onani mutuwo |