Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 65:1 - Buku Lopatulika

1 Mu Ziyoni akulemekezani Inu mwachete, Mulungu, adzakuchitirani Inu chowindachi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 M'Ziyoni akulemekezani Inu mwachete, Mulungu, adzakuchitirani Inu chowindachi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Inu Mulungu, anthu azikutamandani ku Ziyoni, achitedi zimene adalumbira kwa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Matamando akudikira Inu Mulungu mu Ziyoni; kwa inu malumbiro athu adzakwaniritsidwa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 65:1
13 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anakhala m'lingamo; chifukwa chake analitcha mzinda wa Davide.


Ndipo polowa likasa la chipangano la Yehova m'mzinda wa Davide, Mikala mwana wamkazi wa Saulo anasuzumira pazenera, nao mfumu Davide alikutumphatumpha ndi kusewera; ndipo anampeputsa mumtima mwake.


Kwezekani, Yehova, mu mphamvu yanu; potero tidzaimba ndi kulemekeza chilimbiko chanu.


Zowindira Inu Mulungu, zili pa ine, ndidzakuchitirani zoyamika.


Moyo wanga ukhalira chete Mulungu yekha; chipulumutso changa chifuma kwa Iye.


Windani ndipo chitirani Yehova Mulungu wanu zowindazo; onse akumzinga abwere nacho chopereka cha kwa Iye amene ayenera kumuopa.


Msasa wake unali mu Salemu, ndipo pokhala Iye mu Ziyoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa