Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 64:10 - Buku Lopatulika

10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova, nadzakhulupirira Iye; ndipo oongoka mtima onse adzalemekeza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova, nadzakhulupirira Iye; ndipo oongoka mtima onse adzalemekeza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Chauta adalitse anthu ake mtendere ndi chimwemwe zikhale nao, anthu akondwere chifukwa cha Chauta

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Lolani wolungama akondwere mwa Yehova ndi kubisala mwa Iye, owongoka mtima onse atamande Iye!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 64:10
12 Mawu Ofanana  

Olungama achiona nakondwera; ndi osalakwa awaseka pwepwete,


Ndakhulupirira Yehova, mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame?


Mbeu yake idzakhala yamphamvu padziko lapansi; mbadwo wa oongoka mtima udzadalitsidwa.


Sungani moyo wanga, ndilanditseni, ndisakhale nao manyazi, pakuti ndakhulupirira Inu.


Sekerani mwa Yehova, ndimo kondwerani inu olungama mtima; ndipo fuulani mokondwera nonsenu oongoka mtima.


Ndipo anapatsa nyimbo yatsopano m'kamwa mwanga, chilemekezo cha kwa Mulungu wanga; ambiri adzachiona, nadzaopa, ndipo adzakhulupirira Yehova.


Wolungama adzakondwera pakuona kubwezera chilango, adzasamba mapazi ake m'mwazi wa woipa.


Kuunika kufesekera wolungama, ndi chikondwerero oongoka mtima.


Koma kudzitamandira ine konsekonse, iai, koma mu mtanda wa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene mwa Iye dziko lapansi lapachikidwira ine, ndi ine ndapachikidwira dziko lapansi.


Kondwerani mwa Ambuye nthawi zonse: ndibwerezanso kutero, kondwerani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa