Masalimo 64:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anthu onse adzachita mantha; nadzabukitsa chochita Mulungu, nadzasamalira ntchito yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anthu onse adzachita mantha; nadzabukitsa chochita Mulungu, nadzasamalira ntchito yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pompo anthu onse adzachita mantha, adzasimba zimene Mulungu wachita, adzalingalira zomwe Mulungu wachitazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anthu onse adzachita mantha; adzalengeza ntchito za Mulungu ndi kulingalira mozama zomwe Iye wazichita. Onani mutuwo |