Masalimo 64:5 - Buku Lopatulika5 Alimbikitsana m'chinthu choipa; apangana za kutchera misampha mobisika; akuti, Adzaiona ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Alimbikitsana m'chinthu choipa; apangana za kutchera misampha mobisika; akuti, Adzaiona ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Amalimbikira za chiwembu chao, amakambirana zoti atche misampha yobisika, amanena kuti, “Angatiwone ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo amalimbikitsana wina ndi mnzake pa chikonzero chawo choyipa, amayankhula zobisa misampha yawo; ndipo amati, “Adzayiona ndani?” Onani mutuwo |