Masalimo 64:3 - Buku Lopatulika3 Amene anola lilime lao ngati lupanga, napiringidza mivi yao, ndiyo mau akuwawitsa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Amene anola lilime lao ngati lupanga, napiringidza mivi yao, ndiyo mau akuwawitsa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Iwo amanola lilime lao ngati lupanga, amaponya mau obaya ngati mivi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iwo amanola malilime awo ngati malupanga, amaponya mawu awo olasa ngati mivi. Onani mutuwo |