Masalimo 61:8 - Buku Lopatulika8 Potero ndidzaimba zolemekeza dzina lanu kunthawi zonse, kuti ndichite zowinda zanga tsiku ndi tsiku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Potero ndidzaimba zolemekeza dzina lanu kunthawi zonse, kuti ndichite zowinda zanga tsiku ndi tsiku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Motero nthaŵi zonse ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu, tsiku ndi tsiku ndidzachitadi zimene ndidalumbirazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kotero ndidzayimba matamando kwamuyaya pa dzina lanu ndi kukwaniritsa malumbiro anga tsiku ndi tsiku. Onani mutuwo |