Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 61:6 - Buku Lopatulika

6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu. Zaka zake zidzafikira mibadwomibadwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu. Zaka zake zidzafikira mibadwomibadwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Talikitsani moyo wa mfumu, zaka zake zifikire ku mibadwo ndi mibadwo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Wonjezerani masiku a moyo wa mfumu, zaka zake kwa mibado yochuluka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 61:6
7 Mawu Ofanana  

Yehova ndiye gawo la cholowa changa ndi chikho changa, ndinu wondigwirira cholandira changa.


Zingwe zandigwera mondikondweretsa; inde cholowa chokoma ndili nacho.


Anakupemphani moyo, mwampatsa iye; mwamtalikitsira masiku kunthawi za nthawi.


Pakuti mumuikira madalitso kunthawi zonse; mumkondweretsa ndi chimwemwe pankhope panu.


Koma kunakomera Yehova kumtundudza; anammvetsa zowawa; moyo wake ukapereka nsembe yopalamula, Iye adzaona mbeu yake, adzatanimphitsa masiku ake; ndipo chomkondweretsa Yehova chidzakula m'manja mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa