Masalimo 61:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti Inu, Mulungu, mudamva zowinda zanga; munandipatsa cholowa cha iwo akuopa dzina lanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti Inu, Mulungu, mudamva zowinda zanga; munandipatsa cholowa cha iwo akuopa dzina lanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Inu Mulungu, mwamva zimene ndalumbira popemphera. Inu mwandipatsa choloŵa chimene amalandira anthu oopa dzina lanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakuti Inu Mulungu mwamva malumbiro anga; mwandipatsa cholowa cha iwo amene amaopa dzina lanu. Onani mutuwo |