Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 60:9 - Buku Lopatulika

9 Adzandifikitsa ndani m'mzinda wa m'linga? Adzanditsogolera ndani ku Edomu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Adzandifikitsa ndani m'mudzi wa m'linga? Adzanditsogolera ndani ku Edomu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndani adzandifikitse ku mzinda wamalinga? Ndani adzanditsogolere ku Edomu?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Adzandifikitse ndani ku mzinda wotetezedwa? Ndani adzanditsogolera ku Edomu?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 60:9
7 Mawu Ofanana  

Ndodo yachifumu siidzachoka mwa Yuda, kapena wolamulira pakati pa mapazi ake, kufikira atadza Silo; ndipo anthu adzamvera iye.


Ndipo kunali pofikanso chaka, nyengo yakutuluka mafumu, Davide anatumiza Yowabu, pamodzi ndi anyamata ake, ndi Aisraele onse; ndipo iwo anasakaza ana a Amoni, naumangira misasa yankhondo Raba. Koma Davide anatsalira ku Yerusalemu.


Nati Davide, Aliyense woyamba kukantha Ayebusi, yemweyo adzakhala mkulu ndi mtsogoleri. Nayamba kukwerako Yowabu mwana wa Zeruya, nakhala mkulu iyeyu.


Ndipo Kalebe anati, Iye amene akantha mudzi wa Kiriyati-Sefere, naulanda, yemweyo ndidzampatsa Akisa mwana wanga wamkazi akhale mkazi wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa