Masalimo 60:8 - Buku Lopatulika8 Mowabu ndiye mkhate wanga; pa Edomu ndidzaponya nsapato yanga. Filistiya, fuulatu chifukwa cha ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mowabu ndiye mkhate wanga; pa Edomu ndidzaponya nsapato yanga. Filistiya, fuulatu chifukwa cha ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Mowabu adzakhala ngati mbale yosambiramo ine. Edomu adzakhala poponda nsapato zanga. Ndidzafuula mokondwa nditagonjetsa Filistiya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mowabu ndi mbale yanga yosambira, pa Edomu ndidzaponyapo nsapato yanga, pa Filisitiya ndidzafuwula mwakupambana.” Onani mutuwo |