Masalimo 60:7 - Buku Lopatulika7 Giliyadi ndi wanga, Manasenso ndi wanga; ndipo Efuremu ndi mphamvu ya mutu wanga; Yuda ndiye wolamulira wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Giliyadi ndi wanga, Manasenso ndi wanga; ndipo Efuremu ndi mphamvu ya mutu wanga; Yuda ndiye wolamulira wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 “Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanga. Efuremu ali ngati chisoti changa chodzitetezera, Yuda ali ngati ndodo yanga yaufumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanganso; Efereimu ndi chipewa changa chodzitetezera, Yuda ndi ndodo yanga yaufumu Onani mutuwo |