Masalimo 60:1 - Buku Lopatulika1 Mwatitaya Mulungu, mwatipasula; mwakwiya; tibwezereni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mwatitaya Mulungu, mwatipasula; mwakwiya; tibwezereni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu mwatitaya ife, mwatiwonongera otiteteza. Mwatikwiyira, tibwezeni mwakale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Inu Mulungu mwatikanatu ife, ndipo mwatiwonongera otiteteza. Inu mwatikwiyira, tsopano tibwezeretseni mwakale! Onani mutuwo |