Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 59:17 - Buku Lopatulika

17 Ndidzaimbira zakukulemekezani Inu, mphamvu yanga; pakuti Mulungu ndiye msanje wanga, Mulungu wa chifundo changa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndidzaimbira zakukulemekezani Inu, mphamvu yanga; pakuti Mulungu ndiye msanje wanga, Mulungu wa chifundo changa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Inu mphamvu zanga, ndidzakuimbirani nyimbo zokuyamikani, pakuti Inu Mulungu ndinu linga langa, ndinu Mulungu wondiwonetsa chikondi chosasinthika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Inu mphamvu yanga, ndiyimba matamando kwa inu; Inu Mulungu, ndinu linga langa, Mulungu wanga wachikondi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 59:17
7 Mawu Ofanana  

Ndikukondani, Yehova, mphamvu yanga.


Mulungu ndiye pothawirapo pathu ndi mphamvu yathu, thandizo lopezekeratu m'masautso.


Chifukwa chake sitidzachita mantha, lingakhale lisandulika dziko lapansi, angakhale mapiri asunthika, nakhala m'kati mwa nyanja.


Pakuti chifundo chanu nchachikulu kufikira m'mwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.


Kwezekani m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba m'dziko lonse lapansi.


Utsani salimo, bwera nakoni kalingaka, zeze wokondwetsa pamodzi ndi chisakasa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa