Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 57:9 - Buku Lopatulika

9 Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye, ndidzakuimbirani mwa mitundu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye, ndidzakuimbirani mwa mitundu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndidzakuthokozani, Inu Chauta, pakati pa mitundu ya anthu. Ndidzaimba nyimbo zokutamandani pakati pa anthu a maiko onse,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ndidzakutamandani Ambuye, pakati pa mitundu ya anthu, ndidzayimba za Inu pakati pa mayiko.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 57:9
10 Mawu Ofanana  

Ndidzakuyamikani ndi mtima wanga wonse; ndidzaimba zakukulemekezani patsogolo pa milungu.


Chifukwa chake Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu, ndipo dzina lanu ndidzaliimbira.


Aphokoseranji amitundu, nalingiriranji anthu zopanda pake?


Kuti ndipite kufikira guwa la nsembe la Mulungu, kufikira Mulungu wa chimwemwe changa chenicheni, ndi kuti ndikuyamikeni ndi zeze, Mulungu, Mulungu wanga.


Fotokozerani ulemerero wake mwa amitundu; zodabwitsa zake mwa mitundu yonse ya anthu.


ndi kuti anthu a mitundu ina akalemekeze Mulungu, chifukwa cha chifundo; monga kwalembedwa, Chifukwa cha ichi ndidzakuvomerezani Inu pakati pa anthu amitundu, ndidzaimbira dzina lanu.


Galamuka, Debora, galamuka, galamuka, galamuka, unene nyimbo; uka, Baraki, manga nsinga ndende zako, mwana wa Abinowamu, iwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa