Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 57:10 - Buku Lopatulika

10 Pakuti chifundo chanu nchachikulu kufikira m'mwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Pakuti chifundo chanu nchachikulu kufikira m'mwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 pakuti chikondi chanu chosasinthika nchachikulu, chofika mpaka mlengalenga, kukhulupirika kwanu kumafika mpaka ku mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu, kufikira ku mayiko akumwamba; kukhulupirika kwanu kwafika ku mitambo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 57:10
11 Mawu Ofanana  

Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, motero chifundo chake chikulira iwo akumuopa Iye.


Pakuti chifundo chanu nchachikulu kupitirira kumwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.


Alanditsa mfumu yake ndi chipulumutso chachikulu; nachitira chifundo wodzozedwa wake, Davide, ndi mbumba yake, kunthawi zonse.


Yehova, m'mwamba muli chifundo chanu; choonadi chanu chifikira kuthambo.


Ndidzaimbira zakukulemekezani Inu, mphamvu yanga; pakuti Mulungu ndiye msanje wanga, Mulungu wa chifundo changa.


Chilungamo chanunso, Mulungu, chifikira kuthambo; Inu amene munachita zazikulu, akunga Inu ndani, Mulungu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa