Masalimo 57:11 - Buku Lopatulika11 Kwezekani m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba m'dziko lonse lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Kwezekani m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba m'dziko lonse lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Inu Mulungu, onetsani ukulu wanu mumlengalenga monse. Wanditsani ulemerero wanu pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mukwezekedwe Inu Mulungu kuposa mayiko akumwamba, mulole kuti ulemerero wanu ukhale pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwo |