Masalimo 57:8 - Buku Lopatulika8 Galamuka, ulemu wanga; galamukani chisakasa ndi zeze! Ndidzauka ndekha mamawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Galamuka, ulemu wanga; galamukani chisakasa ndi zeze! Ndidzauka ndekha mamawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Lumpha iwe mtima wanga. Inu zeze ndi pangwe, tiyeni lirani, Ndidzadzutsa dzuŵa ndi nyimbo zanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Dzuka moyo wanga! Dzukani zeze ndi pangwe! Ndidzadzuka mʼbandakucha. Onani mutuwo |