Masalimo 57:7 - Buku Lopatulika7 Mtima wanga wakhazikika, Mulungu, ndakhazika mtima; ndidzaimba, inde, ndidzaimba zolemekeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mtima wanga wakhazikika, Mulungu, ndakhazika mtima; ndidzaimba, inde, ndidzaimba zolemekeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Inu Mulungu, mtima wanga wakonzeka, ndithu mtima wanga wakonzekadi. Ndidzaimba nyimbo, nyimbo yake yotamanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mtima wanga ndi wokhazikika, Inu Mulungu mtima wanga ndi wokhazikika. Ndidzayimba nyimbo, nyimbo yake yamatamando. Onani mutuwo |