Masalimo 54:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti alendo andiukira, ndipo oopsa afunafuna moyo wanga; sadziikira Mulungu pamaso pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti alendo andiukira, ndipo oopsa afunafuna moyo wanga; sadziikira Mulungu pamaso pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Anthu onyada andiwukira, anthu ankhalwe amafunafuna moyo wanga, iwo saganizako za Inu Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Alendo akundithira nkhondo; anthu ankhanza akufunafuna moyo wanga, anthu amene salabadira za Mulungu. Onani mutuwo |