Masalimo 54:2 - Buku Lopatulika2 Imvani pemphero langa, Mulungu; tcherani khutu mau a pakamwa panga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Imvani pemphero langa, Mulungu; tcherani khutu mau a pakamwa panga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Inu Mulungu, imvani pemphero langa, tcherani khutu kuti mumve mau a pakamwa panga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Imvani pemphero langa, Inu Mulungu mvetserani mawu a pakamwa panga. Onani mutuwo |