Masalimo 53:4 - Buku Lopatulika4 Kodi ochita zopanda pake sadziwa? Pomadya anthu anga monga akudya mkate; ndipo saitana Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kodi ochita zopanda pake sadziwa? Pomadya anthu anga monga akudya mkate; ndipo saitana Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kani anthu oipaŵa alibe nzeru chotere? Iwo amameza anthu anga, kuŵayesa chakudya, ndipo samutama Mulungu mopemba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kodi anthu ochita zoyipawa adzaphunziradi; anthu amene amadya anthu anga monga mmene anthu amadyera buledi, ndipo sapemphera kwa Mulungu? Onani mutuwo |