Masalimo 53:3 - Buku Lopatulika3 Onse anabwerera; anavunda mtima pamodzi; palibe mmodzi wakuchita bwino, nnena mmodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Onse anabwerera; anavunda mtima pamodzi; palibe mmodzi wakuchita bwino, nnena mmodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma ai anthu onse ndi osokera, onsewo ndi oipa chimodzimodzi. Palibe ndi mmodzi yemwe wochita zabwino, ai, palibiretu ndi mmodzi yemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Aliyense wabwerera, iwo onse pamodzi akhala oyipa; palibe ndi mmodzi yemwe amene amachita chabwino, ngakhale mmodzi. Onani mutuwo |