Masalimo 51:6 - Buku Lopatulika6 Onani, Inu mukondwera ndi zoonadi m'malo a m'katimo; ndipo m'malo a m'tseri mudzandidziwitsa nzeru. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Onani, Inu mukondwera ndi zoonadi m'malo a m'katimo; ndipo m'malo a m'tseri mudzandidziwitsa nzeru. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndithudi, Inu mumakonda mtima woona, choncho mundiphunzitse nzeru zanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Zoonadi inu mumafuna choonadi mu ziwalo zamʼkati mwanga; mumandiphunzitsa nzeru mʼkati mwanga mwenimweni. Onani mutuwo |