Masalimo 51:7 - Buku Lopatulika7 Mundiyeretse ndi hisope ndipo ndidzayera; munditsuke ndipo ndidzakhala wa mbuu woposa matalala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mundiyeretse ndi hisope ndipo ndidzayera; munditsuke ndipo ndidzakhala wa mbu woposa matalala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mundiyeretse ndi hisope ndipo ndidzakhala woyera. Mundisambitse, ndipo ndidzayera kupambana chisanu chambee. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mundiyeretse ndi hisope ndipo ndidzayera, munditsuke ndipo ndidzayera kuposa matalala Onani mutuwo |