Masalimo 5:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika; m'kati mwao m'mosakaza; m'mero mwao ndi manda apululu; lilime lao asyasyalika nalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika; m'kati mwao m'mosakaza; m'mero mwao ndi manda apululu; lilime lao asyasyalika nalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Adani anga amalankhula mabodza okhaokha. Mtima wao umangofuna kuwononga. Mummero mwao muli ngati manda apululu, ndipo lilime lao limalankhula zonyenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Palibe mawu ochokera mʼkamwa mwawo amene angadalirike; mtima wawo wadzaza ndi chiwonongeko. Kummero kwawo kuli ngati manda apululu; ndi lilime lawo amayankhula zachinyengo. Onani mutuwo |