Masalimo 5:8 - Buku Lopatulika8 Yehova, munditsogolere m'chilungamo chanu, chifukwa cha akundizondawo; mulungamitse njira yanu pamaso panga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova, munditsogolere m'chilungamo chanu, chifukwa cha akundizondawo; mulungamitse njira yanu pamaso panga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Inu Chauta, ndinu olungama, munditsogolere pakati pa adani ondizonda. Mundikonzere njira yoongoka kuti ndidzeremo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsogolereni Inu Yehova, mwa chilungamo chanu chifukwa cha adani anga ndipo wongolani njira yanu pamaso panga. Onani mutuwo |