Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 5:2 - Buku Lopatulika

2 Tamvetsani mau a kufuula kwanga, Mfumu yanga, ndi Mulungu wanga; pakuti kwa Inu ndimapemphera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Tamvetsani mau a kufuula kwanga, Mfumu yanga, ndi Mulungu wanga; pakuti kwa Inu ndimapemphera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Imvani kulira kwanga, Inu Mfumu yanga ndi Mulungu wanga, pakuti ndikupempha chithandizo kwa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mverani kulira kwanga kofuna thandizo, Mfumu yanga ndi Mulungu wanga, pakuti kwa Inu, ine ndikupemphera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 5:2
13 Mawu Ofanana  

Koma mucheukire pemphero la kapolo wanu, ndi pembedzero lake, Yehova Mulungu wanga, kumvera kulira ndi kupempha kwake kumene kapolo wanu apempha pamaso panu lero;


Yehova ndiye Mfumu kunthawi yamuyaya; aonongeka amitundu m'dziko lake.


Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu; ndipo ndidzalemekeza dzina lanu kunthawi za nthawi.


Ndifuula kwa Yehova ndi mau anga, ndipo andiyankha m'phiri lake loyera.


Inu ndinu mfumu yanga, Mulungu; lamulirani chipulumutso cha Yakobo.


Wakumva pemphero Inu, zamoyo zonse zidzadza kwa Inu.


Koma Mulungu ndiye mfumu yanga kuyambira kale, wochita zakupulumutsa pakati padziko lapansi.


Mbawanso inapeza nyumba, ndi namzeze chisa chake choikamo ana ake, pa maguwa a nsembe anu, Yehova wa makamu, mfumu yanga ndi Mulungu wanga.


Pakuti Yehova ndiye woweruza wathu, Yehova ndiye wotipatsa malamulo, Yehova ndiye mfumu yathu; Iye adzatipulumutsa.


munamva mau anga; musabise khutu lanu popuma ndi pofuula ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa