Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 5:1 - Buku Lopatulika

1 Mverani mau anga, Yehova, Zindikirani kulingirira kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Mverani mau anga, Yehova, Zindikirani kulingirira kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Imvani mau anga, Inu Chauta, mverani kusisima kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Tcherani khutu ku mawu anga, Inu Yehova, ganizirani za kusisima kwanga

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 5:1
12 Mawu Ofanana  

Yehova, imvani chilungamo, mverani mfuu wanga; tcherani khutu ku pemphero langa losatuluka m'milomo ya chinyengo.


Mau a m'kamwa mwanga ndi maganizo a m'mtima wanga avomerezeke pamaso panu, Yehova, thanthwe langa, ndi Mombolo wanga.


Imvani pemphero langa, Mulungu; tcherani khutu mau a pakamwa panga.


Imvani Mulungu, mau anga, m'kudandaula kwanga; sungani moyo wanga angandiopse mdani.


Mbusa wa Israele, tcherani khutu; inu wakutsogolera Yosefe ngati nkhosa; inu wokhala pa akerubi, walitsani.


Tcherani khutu lanu Yehova, mundiyankhe; pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi.


Ndipo momwemonso Mzimu athandiza kufooka kwathu; pakuti chimene tizipempha monga chiyenera, sitidziwa; koma Mzimu mwini atipempherera ndi zobuula zosatheka kuneneka;


Pakuti maso a Ambuye ali pa olungama, ndi makutu ake akumva pembedzo lao; koma nkhope ya Ambuye ili pa ochita zoipa.


Koma Hana ananena mu mtima; milomo yake inatukula, koma mau ake sanamveke; chifukwa chake Eli anamuyesa woledzera.


Musamandiyesa mdzakazi wanu mkazi woipa; chifukwa kufikira lero ndinalankhula mwa kuchuluka kwa kudandaula kwanga ndi kuvutika kwanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa