Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 5:12 - Buku Lopatulika

12 Pakuti Inu, Yehova, mudzadalitsa wolungamayo; mudzamtchinjiriza nacho chivomerezo ngati chikopa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Pakuti Inu, Yehova, mudzadalitsa wolungamayo; mudzamtchinjiriza nacho chivomerezo ngati chikopa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Inu Chauta, mumadalitsa munthu wochita chilungamo. Kukoma mtima kwanu kuli ngati chishango chomuteteza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ndithu, Inu Yehova, mumadalitsa olungama; mumawazungulira ndi kukoma mtima kwanu ngati chishango.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 5:12
12 Mawu Ofanana  

Aleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, wakukondwera kwambiri ndi malamulo ake.


Adzadalitsa iwo akuopa Yehova, aang'ono ndi aakulu.


M'mahema a olungama muli liu lakufuula mokondwera Dzanja lamanja la Yehova ndi la chipulumutso:


Munditembenukire, ndi kundichitira chifundo, monga mumatero nao akukonda dzina lanu.


Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu, Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendere.


Ndipo Inu Yehova, ndinu chikopa changa; ulemerero wanga, ndi wondiweramutsa mutu wanga.


Chipulumutso ncha Yehova; dalitso lanu likhale pa anthu anu.


Zisoni zambiri zigwera woipa; koma chifundo chidzamzinga iye wakukhulupirira Yehova.


Inu ndinu mobisalira mwanga; m'nsautso mudzandisunga; mudzandizinga ndi nyimbo za chipulumutso.


Imbirani Mulungu, liimbireni nyimbo dzina lake; undirani mseu Iye woberekekayo kuchidikha; dzina lake ndiye Yehova; ndipo tumphani ndi chimwemwe pamaso pake.


Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi chikopa; Yehova adzapatsa chifundo ndi ulemerero; sadzakaniza chokoma iwo akuyenda angwiro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa