Masalimo 48:9 - Buku Lopatulika9 Tidalingalira zachifundo chanu, Mulungu, m'kati mwa Kachisi wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Tidalingalira zachifundo chanu, Mulungu, m'kati mwa Kachisi wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tikakhala m'Nyumba mwanu, Inu Mulungu, timalingalira za chikondi chanu chosasinthika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mʼkati mwa Nyumba yanu Mulungu, ife timalingaliramo zachikondi chanu chosasinthika. Onani mutuwo |