Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 48:5 - Buku Lopatulika

5 Anapenya mudziwo, ndipo pamenepo anadabwa; anaopsedwa, nathawako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Anapenya mudziwo, ndipo pamenepo anadabwa; anaopsedwa, nathawako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Atangopenya mzindawo adadzidzimuka, adachita mantha, nathaŵa chinambalala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 iwo anaona mzindawo ndipo anadabwa kwambiri; anathawa ndi mantha aakulu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 48:5
5 Mawu Ofanana  

Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi, nachita upo akulu pamodzi, Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wake, ndi kuti,


Ndipo anagulula njinga za magaleta ao, nawayendetsa molemetsa; pamenepo Aejipito anati, Tithawe pamaso pa Israele; pakuti Yehova alikuwagwirira nkhondo pa Aejipito.


Ndipo mafumu awa onse anasonkhana, nadza namanga pamodzi ku madzi a Meromu, kumthira Israele nkhondo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa