Masalimo 48:13 - Buku Lopatulika13 Penyetsetsani malinga ake, yesetsani zinyumba zake; kuti mukaziwerengere mibadwo ikudza m'mbuyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Penyetsetsani malinga ake, yesetsani zinyumba zake; kuti mukaziwerengere mibadwo ikudza m'mbuyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Yang'anani bwino machemba ake, penyetsetsani malinga ake, kuti mudzathe kusimbira mbadwo wakutsogolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Yangʼanitsitsani bwino mipanda yake, penyetsetsani malinga ake, kuti mudzafotokoze za izo ku mʼbado wotsatira. Onani mutuwo |