Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 48:12 - Buku Lopatulika

12 Zungulirani Ziyoni, ndipo muuzinge, werengani nsanja zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Zungulirani Ziyoni, ndipo muuzinge, werengani nsanja zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Zungulirani Ziyoni yense, inde zungulirani mzinda wonsewo, ndipo muŵerenge nsanja zake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Yendayendani mu Ziyoni, uzungulireni mzindawo, werengani nsanja zake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 48:12
4 Mawu Ofanana  

Ziyoni anamva nakondwera, nasekerera ana aakazi a Yuda; chifukwa cha maweruzo anu, Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa