Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 47:7 - Buku Lopatulika

7 Pakuti Mulungu ndiye mfumu ya dziko lonse lapansi; imbirani ndi chilangizo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Pakuti Mulungu ndiye mfumu ya dziko lonse lapansi; imbirani ndi chilangizo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Mulungu ndiye Mfumu ya dziko lonse lapansi. Imbani mwaluso nyimbo zotamanda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Pakuti Mulungu ndi mfumu ya dziko lonse lapansi; imbirani Iye salimo la matamando.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 47:7
7 Mawu Ofanana  

Pakuti mkwiyo wake ukhala kanthawi kokha; koma kuyanja kwake moyo wonse. Kulira kuchezera, koma mamawa kuli kufuula kokondwera.


Pakuti Yehova Wam'mwambamwamba ndiye woopsa; ndiye mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.


Mulungu ndiye mfumu ya amitundu, Mulungu akhala pa mpando wachifumu wake woyera.


Ndipo Yehova adzakhala mfumu ya dziko lonse; tsiku lomwelo Yehova adzakhala Iye yekha, ndi dzina lake ilo lokha.


Mau a Khristu akhalitse mwa inu chichulukire mu nzeru yonse, ndi kuphunzitsa ndi kuyambirirana eni okha ndi masalimo, ndi mayamiko ndi nyimbo zauzimu, ndi kuimbira Mulungu ndi chisomo mumtima mwanu.


Ndipo mngelo wachisanu ndi chiwiri anaomba lipenga, ndipo panakhala mau aakulu mu Mwamba, ndi kunena, Ufumu wa dziko lapansi wayamba kukhala wa Ambuye wathu, ndi wa Khristu wake: ndipo adzachita ufumu kufikira nthawi za nthawi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa