Masalimo 47:6 - Buku Lopatulika6 Imbirani Mulungu, imbirani; imbirani mfumu yathu, imbirani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Imbirani Mulungu, imbirani; imbirani mfumu yathu, imbirani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Imbani nyimbo zotamanda Mulungu, imbani nyimbo zotamanda. Imbani nyimbo zotamanda mfumu yathu, imbani nyimbo zotamanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Imbani matamando kwa Mulungu, imbani matamando; imbani matamando kwa mfumu yathu, imbani matamando. Onani mutuwo |