Masalimo 47:3 - Buku Lopatulika3 Atigonjetsera anthu, naika amitundu pansi pa mapazi athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Atigonjetsera anthu, naika amitundu pansi pa mapazi athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Iye adatigonjetsera anthu ambirimbiri, mitundu ina ya anthu adaiika pansi pa ulamuliro wathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye anatigonjetsera mitundu yambirimbiri ya anthu; anayika anthu pansi pa mapazi athu. Onani mutuwo |